Kalozera Wophunzitsira Ndikukonzekera: Zotsatila Za Kalindolondo Wa Pulojekiti
Content type:
OM Training Materials
Author(s):
Julius Nyangaga, Penelop Paliani, Kulimba Chiotcha, Isaac Malunga, the Salvation Army
Theme:
OM Resources: Training Materials
Language:
Chichewa
Published:
8 September 2023
Ntchito ya zotsatira za kalolondolondo wa pulojekiti yakhazikitsidwa kuti isinthe malingalilo athu pa zimene tikufuna kukwanilitsa. Cholinga chake ndikuonetsetsa kuti anthu akumalandila bwanji malingalilo amene tili nawo pa ntchito zimene tikufuna kugwila m’madela awo. Iyi ndi ndondomeko imene ikutiwunikila mmene tingapangile kuti tiyende chitsogolo. Zotsatira za kalolondolondo wa pulojekiti zimapangika pa mkumano ngati uno. Kwa inu alendo izi zimachitika ndi kutheka ngati ku msonkhano uno. Izi zinachitikapo ndi kutheka mmimukumano ina mbuyomu imene inatsogololedwa ndi Sarah Earl, Fred Carden ndi Terry Smutylo mwa ena mmalingalilo oti kumanga ndi kuwunikila ntchito za chitukuko zimene zinatsidikizidwa ndi bugwe la IDRC mchaka cha 2001.
Bukuli linafotokozanso njira zina zimene anthu anasatila malingana ndi kafukufuku amene anachita amene anapeza njira zopitisila pa tsogolo ntchito zachitukuko ndi zotukula dela ndipo izi zidafotokozedwa mwandondomeko imene inagwilitsidwa ntchito pofotokoza zolinga ndi chiyembekezo chawo pa nkumano umene anachita pa nthawi imeneyo.